2 Chronicles 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu adaŵauza kuti, “Mukabwerenso kuno patapita masiku atatu.” Choncho anthuwo adachoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena nao, Mubwerenso atapita masiku atatu. Nachoka anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rehobowamu anayankha kuti, “Mukabwerenso pakapita masiku atatu.” Choncho anthuwo anachoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena nao, Mubwerenso atapita masiku atatu. Nacoka anthu.