2 Chronicles 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Madodawo adamuuza kuti, “Mukaŵachitira chifundo anthu ameneŵa ndi kumaŵasangalatsa, mukalankhula nawo mau abwino, iwowo adzakutumikirani mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena naye, kuti, Mukawachitira chokoma anthu awa, ndi kuwakonda, ndi kulankhula nao mau okoma, adzakhala anyamata anu kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayankha kuti, “Ngati inu muwakomera mtima anthu awa ndi kuwasangalatsa ndiponso kuwayankha mawu abwino, iwo adzakutumikirani nthawi zonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena naye, kuti, Mukawacitira cokoma anthu awa, ndi kuwakonda, ndi kulankhula nao mau okoma, adzakhala anyamata anu kosatha.