2 Chronicles 10:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Rehobowamu adanyozera zimene madoda aja adaamlangiza nakapempha nzeru kwa achinyamata anzake amene adaakula naye pamodzi namamtumikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma analeka uphungu wa akulu akuluwa adampangirawo, nakafunsana ndi anyamata anakula naye pamodzi, oimirira pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Rehobowamu anakana malangizo amene akuluakulu anamupatsa ndipo anakafunsira nzeru kwa anyamata amene anakula naye pamodzi komanso amamutumikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma analeka uphungu wa akulu akuluwa adampangirawo, nakafunsana ndi anyamata anakula naye pamodzi, oimirira pamaso pace.