2 Chronicles 11:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu atafika ku Yerusalemu, adasonkhanitsa ankhondo osankhidwa okwanira 180,000, afuko la Yuda ndi la Benjamini, ndi cholinga akamenyane nkhondo ndi anthu a ku Israele, kuti choncho ambwezere Rehobowamu ufumu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehobowamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu, ndiwo ankhondo, alimbane ndi Aisraele kubwezanso ufumu kwa Rehobowamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rehobowamu atafika ku Yerusalemu anasonkhanitsa asilikali 180,000 a fuko la Yuda ndi Benjamini kuti akachite nkhondo ndi Israeli, kuti abwezeretse ufumu kwa Rehobowamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehabiamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu, ndiwo ankhondo, alimbane ndi Aisrayeli kubwezanso ufumu kwa Rehabiamu.