2 Chronicles 11:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yerobowamu adaadzisankhira ansembe ake, kuti azitumikira ku kachisi ku zitunda, kupembedza mizimu yoipa ndi mafano a atonde ndi a anaang'ombe amene adaŵapanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadziikira ansembe a misanje, ndi a ziwanda, ndi a anaang'ombe adawapanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anasankha ansembe akeake a pa malo opatulika ndi a mafano a mbuzi ndi mwana wangʼombe amene anapanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadziikira ansembe a misanje, ndi a ziwanda, ndi a ana a ng'ombe adawapanga.