2 Chronicles 11:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu adakwatira Mahalati, amene bambo wake anali Yerimoti, mwana wa Davide, ndipo mai wake anali Abihaili mwana wa Eliyabu mwana wa Yese.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Rehobowamu anadzitengera mkazi Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti mwana wa Davide, ndi wa Abihaili mwana wamkazi wa Eliyabu mwana wa Yese;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rehobowamu anakwatira Mahalati, amene abambo ake anali Yerimoti, mwana wa Davide, ndipo amayi ake anali Abihaili, mwana wa Eliabu, mwana wa Yese.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Rehabiamu anadzitengera mkazi Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti mwana wa Davide, ndi wa Abihaili mwana wamkazi wa Eliabu mwana wa Jese;