2 Chronicles 11:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakwatiranso Maaka mwana wa Abisalomu, ndipo adambalira Abiya, Atai, Ziza ndi Selomiti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pambuyo pake anatenga Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu; ndipo anambalira Abiya, ndi Atai, ndi Ziza, ndi Selomiti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anakwatira Maaka, mwana wamkazi wa Abisalomu, amene anamubereka Abiya, Atai, Ziza ndi Selomiti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pambuyo pace anatenga Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu; ndipo anambalira Abiya, ndi Atai, ndi Ziza, ndi Selomiti.