2 Chronicles 11:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu adasankha Abiya, mwana wa Maaka, kuti akhale mtsogoleri pakati pa abale ake, poti ankafuna kuti amlonge ufumu iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Rehobowamu anaika Abiya mwana wa Maaka akhale wamkulu, kalonga mwa abale ake; ndiko kuti adzamlonga ufumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rehobowamu anasankha Abiya mwana wa Maaka kuti akhale mtsogoleri pa abale ake, ndi cholinga choti adzakhale mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Rehabiamu anaika Abiya mwana wa Maaka akhale wamkuru, kalonga mwa abale ace; ndiko kuti adzamlonga ufumu.