2 Chronicles 11:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ukauze Rehobowamu, mwana wa Solomoni, mfumu ya ku Yuda, ndi Aisraele onse a ku Yuda ndi a ku Benjamini kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lankhula ndi Rehobowamu mwana wa Solomoni mfumu ya Yuda ndi Benjamini, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kawuze Rehobowamu mwana wa Solomoni mfumu ya Yuda ndi Aisraeli onse ali mu Yuda ndi Benjamini kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhula ndi Rehabiamu mwana wa Solomo mfumu ya Yuda ndi Benjamini, ndi kuti,