2 Chronicles 12:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mfumu Rehobowamu adapanga zishango zamkuŵa m'malo mwake, nazipereka kwa m'manja mwa akapitao a alonda amene ankalonda pakhomo pa nyumba ya mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Rehobowamu mfumu anapanga m'malo mwa izi zikopa zamkuwa, nazipereka m'manja mwa kapitao wa olindirira akusunga pakhomo pa nyumba ya mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mfumu inapereka zishango zamkuwa kwa oyangʼanira mʼmalo mwake ndipo iwo anazipereka kwa oyangʼanira alonda amene amayangʼanira pa chipata cha nyumba yaufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Rehabiamu mfumu anapanga m'malo mwa izo zikopa zamkuwa, nazipereka m'manja mwa kapitao wa olindirira akusunga pakhomo pa nyumba ya mfumu.