2 Chronicles 12:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe adzakhala akapolo a Sisakeyo, kuti anthuwo adziŵe kusiyanitsa pakati pa kutumikira Ine ndi kutumikira mafumu a maiko achilendo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma adzakhala akapolo ake, kuti adziwe kunditumikira kwanga, ndi kuwatumikira kwa maufumu a maiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe iwo adzakhala pansi pa ulamuliro wake, kuti aphunzire kudziwa kusiyanitsa pakati pa kutumikira Ine ndi kutumikira mafumu a mayiko ena.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adzakhala akapolo ace, kuti adziwe kunditumikira kwanga, ndi kuwatumikira kwa maufumu a maiko.