2 Chronicles 13:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka cha 18 cha ufumu wa Yerobowamu, Abiya adaloŵa ufumu wa ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yerobowamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Yeroboamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yerobiamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.