2 Chronicles 13:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kunena za ife, Chauta ndiye Mulungu wathu, ndipo sitidamsiye ai. Tili nawo ansembe, ana a Aaroni, otumikira Chauta, tilinso ndi Alevi amene amatumikira ansembewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, sitinamsiya Iye; ndi ansembe tili nao akutumikira Yehova ana a Aroni, ndi Alevi, m'ntchito mwao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma kunena za ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, ndipo sitinamusiye. Ansembe amene amatumikira Yehova ndi ana a Aaroni ndipo amathandizidwa ndi Alevi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, sitinamsiya Iye; ndi ansembe tiri nao akutumikira Yehova ana a Aroni, ndi. Alevi, m'nchito mwao,