2 Chronicles 13:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Yuda aja poyang'ana, adangoona kuli nkhondo kutsogolo kwao ndi kumbuyo komwe. Tsono adafuula kwa Chauta, ndipo ansembe adayamba kuliza malipenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pocheuka Yuda, taonani, nkhondo inayambana nao kumaso ndi kumbuyo; nafuulira iwo kwa Yehova, ndi ansembe analiza malipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asilikali a Yuda anatembenuka ndipo anaona kuti nkhondo imachitikira kutsogolo ndi kumbuyo. Ndipo iwo anafuwulira Yehova. Ansembe anayimba malipenga awo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo poceuka Yuda, taonani, nkhondo inayambana nao kumaso ndi kumbuyo; napfuulira iwo kwa Yehova, ndi ansembe analiza malipenga.