2 Chronicles 13:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abiya pamodzi ndi anthu ake adapha Aisraelewo, kupha kwake kwakukulu. Adaphedwa Aisraele okwanira 500,000, anthu ndithu osankhidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abiya ndi anthu ake anawakantha makanthidwe akulu; nagwa, nafa amuna osankhika zikwi mazana asanu a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abiya pamodzi ndi anthu ake anapha anthu ambiri, kotero kuti Aisraeli 500,000 odziwa bwino nkhondo anaphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abiya ndi anthu ace anawakantha makanthidwe akuru; nagwa, nafa amuna osankhika zikwi mazanaasanu a Israyeli.