2 Chronicles 13:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Abiya mphamvu zake zidakula. Ndipo adakwatira akazi khumi ndi anai, nabala ana aamuna 22 ndi ana aakazi 16.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Abiya anakula mphamvu, nadzitengera akazi khumi ndi anai, nabala ana amuna makumi awiri mphambu awiri, ndi ana akazi khumi mphamvu asanu ndi mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Abiya mphamvu zake zinakula. Iye anakwatira akazi 14 ndipo anali ndi ana aamuna 22 ndi ana aakazi 16.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Abiya anakula mphamvu, nadzitengera akazi khumi ndi anai, nabala ana amuna makumi awiri mphambu awiri, ndi ana akazi khumi mphambu asanu ndi mmodzi.