2 Chronicles 13:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi simukudziŵa kuti Chauta, Mulungu wa Israele, adapereka ufumu wa Israele kwa Davide ndi kwa ana ake mpaka muyaya, pochita chipangano chosaphwanyika?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
simudziwa kodi kuti Yehova Mulungu wa Israele anapereka chiperekere ufumu wa Israele kwa Davide, kwa iye ndi ana ake, ndi pangano lamchere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi inu simukudziwa kuti Yehova, Mulungu wa Israeli, wapereka ufumu wa Israeli kwa Davide ndi zidzukulu zake mpaka muyaya ndiponso pangano la mchere?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
simudziwa kodi kuti Yehova Mulungu wa Israyeli anapereka ciperekere ufumu wa Israyeli kwa Davide, kwa iye ndi ana ace, ndi pangano la mcere?