2 Chronicles 13:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Yerobowamu mwana wa Nebati, mtumiki wa Solomoni mwana wa Davide, adanyamuka naukira mbuyakeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yerobowamu mwana wa Nebati mnyamata wa Solomoni mwana wa Davide anauka, napandukana ndi mbuye wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Yeroboamu mwana wa Nebati, mtumiki wa Solomoni mwana wa Davide, anawukira mbuye wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yerobiamu mwana wa Nebati mnyamata wa Solomo mwana wa Davide anauka, napandukana ndi mbuye wace.