2 Chronicles 15:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo adasonkhana ku Yerusalemu pa mwezi wachitatu chaka cha 15 cha ufumu wa Asa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anasonkhana ku Yerusalemu mwezi wachitatu, Asa atakhala mfumu zaka khumi ndi zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anasonkhana mu Yerusalemu mwezi wachitatu wa chaka cha 15 cha ulamuliro wa Asa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anasonkhana ku Yerusalemu mwezi wacitatu, Asa atakhala mfumu zaka khumi ndi zinai.