2 Chronicles 15:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaamvana kuti aliyense wosafunafuna Chauta, Mulungu wa Israele, aziphedwa, kaya ndi wamng'ono kaya wamkulu, wamwamuna kapena wamkazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti yense wosafuna Yehova Mulungu wa Israele aphedwe, ngakhale wamng'ono kapena wamkulu, wamwamuna kapena wamkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wosafunafuna Yehova Mulungu wa Israeli aziphedwa, kaya ndi wamngʼono kapena wamkulu, mwamuna kapena mkazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti yense wosafuna Yehova Mulungu wa Israyeli aphedwe, ngakhale wamng'ono kapena wamkuru, wamwamuna kapena wamkazi.