2 Chronicles 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi adalumbira kwa Chauta mokweza mau ndi mofuula, alikuliza malipenga ndi mbetete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analumbira kwa Yehova ndi mau akulu, ndi kufuula ndi mphalasa ndi malipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo analumbira kwa Yehova, mokweza mawu, akuyimba malipenga ndi mbetete.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analumbira kwa Yehova ndi mau akuru, ndi kupfuula ndi mphalasa ndi malipenga.