2 Chronicles 15:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akachisi sadaŵaononge ku Israele. Ngakhale zinali choncho, mtima wa Asa udakhala wangwiro masiku onse a moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana misanje siinachotsedwa m'Israele, mtima wa Asa unali wangwiro masiku ake onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale kuti sanachotse malo opembedzerako mafano mu Israeli, mtima wa Asa unali wodzipereka kwathunthu kwa Yehova, masiku onse a moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana misanje siinacotsedwa m'Israyeli, mtima wa Asa unali wangwiro masiku ace onse.