2 Chronicles 15:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi yaitali Aisraele adakhala opanda Mulungu woona, ndiponso opanda wansembe woŵaphunzitsa, ndipo analibe malamulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku ambiri tsono Israele anakhala wopanda Mulungu woonayo, ndi wopanda wansembe wakuphunzitsa, ndi wopanda chilamulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa nthawi yayitali Israeli anali wopanda Mulungu weniweni, wopanda wansembe wophunzitsa ndi wopanda malamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku ambiri tsono Israyeli anakhala wopanda Mulungu woonayo, ndi wopanda wansembe wakuphunzitsa, ndi wopanda cilamulo;