2 Chronicles 15:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene anali pa mavuto, namabwera kudzafunafuna Chauta, Mulungu wa Israele, ankamupeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma pamene anatembenukira kwa Yehova Mulungu wa Israele m'kusautsidwa kwao, ndi kumfuna, anampeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene anali pa mavuto anatembenukira kwa Yehova, Mulungu wa Israeli ndi kufunafuna Iye, ndipo anamupeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma pamene anatembenukira kwa Yehova Mulungu wa Israyeli m'kusautsidwa kwao, ndi kumfuna, anampeza.