2 Chronicles 15:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo adagalukirana, mtundu wina unkamenyana ndi mtundu wina, mzinda unkamenyana ndi mzinda wina, pakuti Mulungu adaaŵavuta ndi mazunzo osiyanasiyana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapasulidwa, mtundu wa anthu kupasula unzake, ndi mudzi kupasula mudzi; pakuti Mulungu anawavuta ndi masautso ali onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtundu umodzi umakanthidwa ndi mtundu wina ndipo mzinda wina umakanthidwa ndi mzinda wina, pakuti Mulungu amawasautsa ndi mazunzo a mtundu uliwonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapasulidwa, mtundu wa anthu kupasula unzace, ndi mudzi kupasula mudzi; pakuti Mulungu anawabvuta ndi masautso ali onse.