2 Chronicles 15:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu limbani mtima, manja anu asafooke chifukwa mudzalandira mphotho ya ntchito yanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma limbikani inu, manja anu asalende; pakuti ku ntchito yanu kuli mphotho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu, khalani amphamvu ndipo musataye mtima, pakuti mudzalandira mphotho ya ntchito yanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma limbikani inu, manja anu asalende; pakuti ku nchito yanu kuli mphotho.