2 Chronicles 16:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Asa adapsera mtima mneneriyo, ndipo adammanga namuika m'ndende, popeza kuti adaakwiya naye kwambiri chifukwa cha zimenezi. Kenaka Asayo adayamba kuchita zankhalwe pa anthu enanso nthaŵi yomweyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Asa anakwiya naye mlauliyo, namuika m'kaidi; pakuti adapsa mtima naye chifukwa cha ichi. Nthawi yomweyi Asa anasautsa anthu ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asa anamupsera mtima mlosi uja chifukwa cha izi mwakuti anakwiya kwambiri namuyika mʼndende. Pa nthawi yomweyonso Asa anazunza mwankhanza anthu ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Asa anakwiya naye mlauliyo, namuika m'kaidi; pakuti adapsa mtima naye cifukwa ca ici. Nthawi yomweyi Asa anasautsa anthu ena.