2 Chronicles 16:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adamwalira, pa chaka cha 41 cha ufumu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Asa ndi makolo ake, namwalira atakhala mfumu zaka makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mʼchaka cha 41 cha ufumu wake, Asa anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Asa ndi makolo ace, namwalira atakhala mfumu zaka makumi anai.