2 Chronicles 16:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Aetiopiya ndi Alibiya sanali gulu lalikulu lankhondo, lokhala ndi magaleta ochuluka ndiponso anthu ambirimbiri okwera pa akavalo? Komabe chifukwa chodalira Chauta, Chautayo adaŵapereka kwa inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga Akusi ndi Alibiya, sanakhale khamu lalikulukulu, ndi magaleta ndi apakavalo ambirimbiri, koma muja munatama Yehova anawapereka m'dzanja mwanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Akusi ndi Alibiya sanali gulu lankhondo lamphamvu lokhala ndi magaleta ochuluka ndi okwera magaleta ake? Koma pamene inu munadalira Yehova, Iye anawapereka mʼdzanja lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanga Akusi ndi Alubi, sanakhala khamu lalikurukuru, ndi magareta ndi apakavalo ambirimbiri, koma muja munatama Yehova anawapereka m'dzanja mwanu?