2 Chronicles 17:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehosafati, mwana wa Asa, adaloŵa ufumu m'malo mwa bambo wake, ndipo adadzilimbitsa pofuna kulimbana ndi Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehosafati mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake, nadzilimbitsa kuyambana ndi Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehosafati mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake ndipo anadzilimbitsa pofuna kulimbana ndi Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehosafati mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace, nadzilimbitsa kuyambana ndi Israyeli.