2 Chronicles 17:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mphamvu za Yehosafati zidanka zikulirakulira. Ku Yuda adamanga malinga ndi mizinda yosungirako zinthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehosafati anakula chikulire, namanga m'Yuda nyumba zansanja, ndi midzi ya chuma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu za Yehosafati zinkakulirakulira. Iye anamanga malo otetezedwa ndi mizinda yosungiramo chuma mu Yuda
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehosafati anakula cikulire, namanga m'Yuda nyumba zansanja, ndi midzi ya cuma.