2 Chronicles 17:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho anali ndi nyumba zikuluzikulu zosungiramo zinthu ku mizinda ya ku Yuda. Ku Yerusalemu anali ndi ankhondo, anthu amphamvu ndi olimba mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakhala nazo ntchito zambiri m'midzi ya Yuda, ndi anthu a nkhondo, ngwazi zamphamvu m'Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anali ndi katundu wambiri mʼmizinda ya Yuda. Iye anayikanso asilikali odziwa bwino nkhondo mu Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakhala nazo nchito zambiri m'midzi ya Yuda, ndi anthu a nkhondo, ngwazi zamphamvu m'Yerusalemu.