2 Chronicles 17:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasiya mwana wa Zikiri, mtsogoleri wotsatana naye, amene adaadzipereka mwaufulu ku ntchito ya Chauta, anali ndi anthu amphamvu ndi olimba mtima 200,000. (Amasiya adadzipereka kutumikira Ambuye.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wotsatana naye Amasiya mwana wa Zikiri, wodzipereka kwa Yehova mwaufulu, ndi pamodzi ndi iye ngwazi zamphamvu zikwi mazana awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
otsatana naye, Amasiya mwana wa Zikiri amene anadzipereka yekha kutumikira Yehova, anali ndi anthu 200,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wotsatana naye Amasiya mwana wa Zikri, wodzipereka kwa Yehova mwaufulu, ndi pamodzi ndi iye ngwazi zamphamvu zikwi mazana awiri;