2 Chronicles 17:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa ndiwo ankatumikira mfumu, pamodzi ndi ena amene mfumu idaŵaika ku mizinda yamalinga ku dziko lonse la Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiwo amene analindirira mfumu, osawerenga iwo aja mfumu adawaika m'midzi yamalinga m'Yuda monse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi anthu amene ankatumikira mfumu osawerengera amene anawayika mʼmizinda yotetezedwa mʼdziko lonse la Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiwo amene analindirira mfumu, osawerenga iwo aja mfumu adawaika m'midzi yamalinga m'Yuda monse.