2 Chronicles 17:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chachitatu cha ufumu wake, Yehosafati adatuma nduna zake, Benihali, Obadiya, Zekariya, Netanele ndi Mikaya, kuti akaphunzitse ku mizinda ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chachitatu cha ufumu wake anatuma akalonga ake, ndiwo Benihayili, ndi Obadiya, ndi Zekariya, ndi Netanele, ndi Mikaya, aphunzitse m'midzi ya Yuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chachitatu cha ufumu wake, iye anatuma akuluakulu ake Beni-Haili, Obadiya, Zekariya, Netaneli ndi Mikaya kukaphunzitsa mʼmizinda ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cacitatu ca ufumu wace anatuma akalonga ace, ndiwo Benihayili, ndi Obadiya, ndi Zekariya, ndi Netaneli, ndi Mikaya, aphunzitse m'midzi ya Yuda;