2 Chronicles 17:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankaphunzitsa ku Yuda, ali ndi buku la malamulo a Chauta. Ndipo adayendera mizinda yonse ya ku Yuda, namaphunzitsa pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaphunzitsa m'Yuda ali nalo buku la chilamulo la Yehova, nayendayenda m'midzi yonse ya Yuda, naphunzitsa mwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anaphunzitsa mu Yuda monse atatenga Buku la Malamulo a Yehova iwo anayenda mʼmizinda yonse ya ku Yuda ndipo anaphunzitsa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaphunzitsa m'Yuda ali nalo buku la cilamulo la Yehova, nayendayenda m'midzi yonse ya Yuda, naphunzitsa mwa anthu.