2 Chronicles 18:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mikaya adati, “Pali Chauta wamoyo, zimene Mulungu wanga andiuze, ndizo ndidzalankhule.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Mikaya, Pali Yehova, chonena Mulungu wanga ndidzanena chomwechi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mikaya anati, “Pali Yehova wamoyo, ine ndidzanena zimene Mulungu wanga andiwuze.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Mikaya, Pali Yehova, conena Mulungu wanga ndidzanena comweci.