2 Chronicles 18:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mfumuyo idamufunsa kuti, “Kodi ndikulumbiritse kangati, kuti undiwuze zoona zokhazokha m'dzina la Chauta?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inati naye, Ndikulumbiritse kangati kuti unene nane choonadi chokhachokha m'dzina la Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inati kwa iye, “Kodi ndikuwuze kangati kuti ulumbire kuti usandiwuze chilichonse koma zoonadi mʼdzina la Yehova?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inati naye, Ndikulumbiritse kangati kuti unene nane coonadi cokha cokha m'dzina la Yehova?