2 Chronicles 18:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mfumu ya ku Israele adauza Yehosafati kuti, “Suja ndidaakuuzani kuti ameneyu sadzandilosera zabwino koma zoipa zokha?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Israele inati kwa Yehosafati, Sindinakuuzani kuti sadzandinenera zabwino koma zoipa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ya Israeli inati kwa Yehosafati, “Kodi ine sindinakuwuzeni kuti sandinenera zabwino koma zoyipa zokhazokha?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Israyeli inati kwa Yehosafati, Sindinakuuzani kuti sadzandinenera zabwino koma zoipa?