2 Chronicles 18:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsonotu ngati Chauta waika mzimu wabodza m'kamwa mwa aneneri anuŵa, ndiye kuti Iye yemwe waneneratu kuti mukaona tsoka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsono taonani, Yehova analonga mzimu wabodza m'kamwa mwa aneneri anu awa, nakunenetserani choipa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho Yehova wayika mzimu wabodza mʼkamwa mwa aneneri anuwa. Yehova waneneratu kuti inu mukaona tsoka.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsono taonani, Yehova analonga mzimu wabodza m'kamwa mwa aneneri anu awa, nakunenetserani coipa Yehova.