2 Chronicles 18:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mikaya adati, “Udzadziŵa pa tsiku limene uzikaloŵa m'chipinda china ndi china cham'kati kuti ukabisale.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Mikaya, Tapenya, udzaona tsiku lolowa iwe m'chipinda cham'kati kubisala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikaya anayankha kuti, “Udzadziwa pa tsiku limene uzikalowa mʼchipinda chamʼkati kuti ukabisale.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Mikaya, Tapenya, udzaona tsiku lolowa iwe m'cipinda cam'kati kubisala.