2 Chronicles 18:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Ahabu, mfumu ya ku Israele, adati, “Mgwireni Mikayayu, mupite naye kwa Amoni, mkulu wa mzinda, ndiponso kwa Yowasi mwana wa mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Israele inati, Mumtenge Mikaya, mukambweze kwa Amoni kazembe wa mudzi, ndi kwa Yowasi mwana wa mfumu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mfumu ya Israeli inalamula kuti, “Tengani Mikaya ndipo mupite naye kwa Amoni, wolamulira mzindawo ndi kwa Yowasi mwana wa mfumu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Israyeli inati, Mumtenge Mikaya, mukambweze kwa Amoni kazembe wa mudzi, ndi kwa Yoasi mwana wa mfumu;