2 Chronicles 18:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukaŵauze mau angaŵa akuti, ‘Munthu uyu muikeni m'ndende, ndipo muzimpatsa chakudya pang'ono ndi madzi pang'ono, mpaka ine nditabwerera mwamtendere.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nimuziti, Itero mfumu, Mumuike uyu m'kaidi, ndi kumdyetsa chakudya chomsautsa, ndi kumwetsa madzi omsautsa, mpaka ndikabwera mumtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mukanene kuti, ‘Chimene mfumu ikunena ndi ichi; Muyike munthu uyu mʼndende ndipo musamupatse kanthu kalikonse koma buledi ndi madzi pangʼono mpaka nditabwera mwamtendere.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nimuziti, Itero mfumu, Mumuike uyu m'kaidi, ndi kumdyetsa cakudya comsautsa, ndi kummwetsa madzi omsautsa, mpaka ndikabwera mumtendere.