2 Chronicles 19:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe pali zina zabwino zimene mudachita, pakuti mudaononga mafano a m'dziko muno, ndipo mwakhala mukulimbikira ndi mtima wonse kufunafuna Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zapezeka zokoma mwa inu, popeza mwazichotsa zifanizo m'dzikomo, mwalunjikitsanso mtima wanu kufuna Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe, muli zinthu zina zabwino mwa inu, pakuti inu mwachotsa mʼdziko muno mafano a Asera ndipo mwakhazikitsa mtima wanu pa kufunafuna Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zapezeka zokoma mwa inu, popeza mwazicotsa zifanizo m'dzikomo, mwaluniikitsanso mtima wanu kufuna Mulungu.