2 Chronicles 19:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika anthu oweruza m'dzikomo, mu mzinda uliwonse wamalinga wa ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naika oweruza m'dziko, m'midzi yonse yamalinga ya m'Yuda, mudzi ndi mudzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasankha oweruza mʼdzikomo, mu mzinda uliwonse wotetezedwa wa Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naika oweruza m'dziko, m'midzi yonse yamalinga ya m'Yuda, m'mudzi m'mudzi;