2 Chronicles 19:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adauza aweruziwo kuti, “Muganize bwino zimene mukuchita, pakuti simukuweruza m'dzina la munthu ai, koma m'dzina la Chauta. Chautayo ali nanu pamene mukuweruza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati kwa oweruza, Khalani maso umo muchitira; pakuti simuweruzira anthu koma Yehova; ndipo ali nanu Iyeyu pakuweruza mlandu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anawawuza kuti, “Muganize bwino zimene mukuchita, chifukwa simukuweruza mʼmalo mwa munthu koma Yehova, amene ali nanu pamene mukupereka chiweruzo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati kwa oweruza, Khalani maso umo mucitira; pakuti simuweruzira anthu koma Yehova; ndipo ali nanu Iyeyu pakuweruza mlandu.