2 Chronicles 19:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵalamula kuti, “Muzichita ntchito imeneyi moopa Chauta, mokhulupirika, ndiponso ndi mtima wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawalangiza, ndi kuti, Muzitero ndi kuopa Yehova mokhulupirika ndi mtima wangwiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawalamula kuti, “Inu mutumikire mokhulupirika ndi mtima wanu wonse moopa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawalangiza, ndi kuti, Muzitero ndi kuopa Yehova mokhulupirika ndi mtima wangwiro.