2 Chronicles 20:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano chimene akutibwezera nkudzatipirikitsa m'dziko limene Inu mudatipatsa kuti likhale choloŵa chathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tapenyani, m'mene atibwezera, kudzatiinga m'cholowa chanu, chimene munatipatsa chikhale cholowa chathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, mmene akutibwezera ife pobwera kudzatithamangitsa mʼdziko limene inu munatipatsa ngati cholowa chathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tapenyani, m'mene atibwezera; kudzatiinga m'colowa canu, cimene munatipatsa cikhale colowa cathu.