2 Chronicles 20:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo nkuti anthu onse a dziko la Yuda ataimirira pamaso pa Chauta, pamodzi ndi akazi ao ndi ana ao ndi ang'onoang'ono omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ayuda onse anakhala chilili pamaso pa Yehova, pamodzi ndi makanda ao, akazi ao, ndi ana ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse a Yuda, pamodzi ndi akazi awo ndi ana ndi makanda, anayima chilili pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ayuda onse anakhala ciriri pamaso pa Yehova, pamodzi ndi makanda ao, akazi ao, ndi ana ao.