2 Chronicles 20:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mumsonkhanomo mzimu wa Chauta udatsikira Yehaziele, mwana wa Zekariya, mwana wa Benaya, mwana wa Yeiyele, mwana wa Mataniya, mlevi, mmodzi mwa ana a Asafu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mzimu wa Yehova unagwera Yahaziele mwana wa Zekariya, mwana wa Benaya, mwana wa Yeiyele, mwana wa Mataniya, Mlevi, wa ana a Asafu, pakati pa msonkhano;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mzimu wa Yehova unabwera pa Yahazieli mwana wa Zekariya, mwana wa Benaya, mwana wa Yeiyeli, mwana wa Mataniya Mlevi, chidzukulu cha Asafu, atayimirira mu msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mzimu wa Yehova unagwera Yahazieli mwana wa Zekriya, mwana wa Benaya, mwana wa Yetieli, mwana wa Mataniya, Mlevi, wa ana a Asafu, pakati pa msonkhano;